Genesis 1:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo panali madzulo ndipo panali m'mawa, tsiku lachinai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo panali madzulo ndipo panali m'mawa, tsiku lachinai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Ndipo kudali madzulo ndiponso m'maŵa, tsiku lachinai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Ndipo panali madzulo ndiponso mmawa pa tsiku lachinayi. Onani mutuwo |