Filemoni 1:8 - Buku Lopatulika8 Momwemo, ndingakhale ndili nako kulimbika mtima kwakukulu mu Khristu kukulamulira chimene chiyenera, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Momwemo, ndingakhale ndili nako kulimbika mtima kwakukulu m'Khristu kukulamulira chimene chiyenera, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tsono, inde nkotheka kuti ndichite kukulamula m'dzina la Khristu zimene uyenera kuchita. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Tsopano ngakhale kuti mwa Khristu nditha kulimba mtima ndi kulamulira kuti uchite zimene uyenera kuchita, Onani mutuwo |