Ezara 3:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo anakhazika guwa la nsembe patsinde pake chifukwa cha kuopa iwo anthu a m'maikomo; nakwezera Yehova nsembe zopsereza pamenepo, nsembe zopsereza zam'mawa ndi zamadzulo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo anakhazika guwa la nsembe patsinde pake chifukwa cha kuopa iwo anthu a m'maikomo; nakwezera Yehova nsembe zopsereza pamenepo, nsembe zopsereza zam'mawa ndi zamadzulo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ngakhale kuti ankaopa mitundu ina ya anthu am'maikowo, adamanga guwalo pa maziko ake akale, ndipo ankapereka nsembe zopsereza kwa Chauta paguwapo m'maŵa ndi madzulo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ndi mantha ndi mantha chifukwa cha anthu a mʼmayikomo, iwo anamanga guwalo pa maziko ake akale, ndipo anapereka nsembe zopsereza kwa Mulungu pa guwapo mmawa ndi madzulo. Onani mutuwo |