Eksodo 9:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo thonje ndi barele zinayoyoka; pakuti barele lidafula, ndi thonje lidayamba maluwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo thonje ndi barele zinayoyoka; pakuti barele lidafula, ndi thonje lidayamba maluwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Ndipo thonje lidaonongeka pamodzi ndi barele yemwe, chifukwa choti bareleyo anali atacha, ndipo thonjelo linali ndi nkhunje. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Thonje ndi barele zinawonongeka, popeza barele anali atakhwima ndi thonje linali ndi maluwa. Onani mutuwo |