Eksodo 9:12 - Buku Lopatulika12 Koma Yehova analimbitsa mtima wa Farao, kuti sanamvere iwo; monga Yehova adalankhula ndi Mose. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Koma Yehova analimbitsa mtima wa Farao, kuti sanamvere iwo; monga Yehova adalankhula ndi Mose. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Koma Mulungu adamuumitsa mtima Farao, ndipo Faraoyo sadaŵalole anthuwo kuti apite monga momwe Chauta adaauzira Mose muja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Koma Yehova anawumitsa mtima wa Farao ndipo iye sanamvere Mose ndi Aaroni monga momwe Yehova anamuwuzira Mose. Onani mutuwo |