Eksodo 9:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo alembi sanathe kuima pamaso pa Mose chifukwa cha zilondazo; popeza panali zilonda pa alembi ndi pa Aejipito onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo alembi sanakhoza kuima pamaso pa Mose chifukwa cha zilondazo; popeza panali zilonda pa alembi ndi pa Aejipito onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Amatsenga aja sadathenso kufika pamaso pa Mose chifukwa iwonso anali ndi zithupsa zokhazokha, monga Aejipito onse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Amatsenga sanathe kumuyandikira Mose chifukwa nawonso anali ndi zithupsa monga mmene analili Aigupto ena onse. Onani mutuwo |