Eksodo 9:1 - Buku Lopatulika1 Pamenepo Yehova anati kwa Mose, Lowa kwa Farao, numuuze, Atero Yehova Mulungu wa Ahebri, Lola anthu anga amuke, kuti anditumikire. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Pamenepo Yehova anati kwa Mose, Lowa kwa Farao, numuuze, Atero Yehova Mulungu wa Ahebri, Lola anthu anga amuke, kuti anditumikire. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pambuyo pake Chauta adalamula Mose kuti, “Pita kwa Farao ukamuuze kuti, ‘Chauta, Mulungu wa Ahebri, akunena kuti uŵalole anthu anga apite akandipembedze. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Kenaka Yehova anati kwa Mose, “Pita kwa Farao ndipo ukamuwuze kuti Yehova, Mulungu wa Ahebri akuti alole anthu anga apite kuti akandipembedze. Onani mutuwo |