Eksodo 8:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo alembi anachita momwemo ndi matsenga ao, nakweretsa achule padziko la Ejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo alembi anachita momwemo ndi matsenga ao, nakweretsa achule pa dziko la Ejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Koma amatsenga aja nawonso adapanga ao achule ndipo adayamba kukwera pa mtunda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Koma amatsenga anachita zinthu zomwezo mʼmatsenga awo. Iwonso anatulutsa achule mʼdziko lonse la Igupto. Onani mutuwo |