Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 8:7 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Koma amatsenga anachita zinthu zomwezo mʼmatsenga awo. Iwonso anatulutsa achule mʼdziko lonse la Igupto.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

7 Ndipo alembi anachita momwemo ndi matsenga ao, nakweretsa achule padziko la Ejipito.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndipo alembi anachita momwemo ndi matsenga ao, nakweretsa achule pa dziko la Ejipito.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Koma amatsenga aja nawonso adapanga ao achule ndipo adayamba kukwera pa mtunda.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 8:7
8 Mawu Ofanana  

Naye Farao anayitanitsa anthu ake anzeru ndi amatsenga, ndipo nawonso amatsenga a Chiigupto anachita zinthu zomwezo mwa matsenga awo.


Koma amatsenga a Chiigupto anachita zinthu zomwezo mwa matsenga awo. Choncho Farao anawumabe mtima, ndipo sanamvere zonena za Mose ndi Aaroni monga momwe Yehova ananeneratu.


Koma amatsenga atayesa kupanga nsabwe mwa matsenga awo, analephera. Ndipo nsabwezo zinali pa munthu aliyense ndi pa ziweto zawo.


Chifukwa akhristu onama ndi aneneri onama adzaoneka ndipo adzachita zizindikiro zazikulu ndi zodabwitsa kuti akanyenge ngakhale osankhidwawo ngati kukanakhala kotheka kutero.


Monga momwe Yanesi ndi Yambere anawukira Mose, momwemonso anthu amenewa amawukira choonadi. Nzeru zawo ndi zowonongeka ndipo pa za chikhulupiriro, ndi okanidwa.


Chifukwa cha zizindikiro zimene chinaloledwa kuchita mʼmalo mwa chirombo choyamba chija, chimene bala lake linapola, chinanyenga anthu okhala pa dziko lapansi. Chinalamula anthu kuti apange fano mopereka ulemu kwa chirombo chimene chinavulazidwa ndi lupanga, koma nʼkukhalabe ndi moyo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa