Eksodo 8:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo ndidzaika chosiyanitsa pakati pa anthu anga ndi anthu ako; mawa padzakhala chizindikiro ichi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo ndidzaika chosiyanitsa pakati pa anthu anga ndi anthu ako; mawa padzakhala chizindikiro ichi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Ndidzasiyanitsa ndithu pakati pa anthu anga ndi anthu ako. Chozizwitsa chimenechi chichitika maŵali.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Ndidzasiyanitsa pakati pa anthu anga ndi anthu ako. Chizindikiro chozizwitsa ichi chidzachitika mawa.” Onani mutuwo |