Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 7:25 - Buku Lopatulika

25 Ndipo anafikira masiku asanu ndi awiri atapanda mtsinje Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Ndipo anafikira masiku asanu ndi awiri atapanda nyanja Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Padapita masiku asanu ndi aŵiri, Chauta ataipitsa mtsinje uja.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Panapita masiku asanu ndi awiri Yehova atamenya madzi a mu mtsinje wa Nailo.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 7:25
5 Mawu Ofanana  

Chomwecho Gadi anafika kwa Davide, namuuza nanena naye, Kodi zikugwereni m'dziko mwanu zaka zisanu ndi ziwiri za njala? Kapena muthawe adani anu akukupirikitsani miyezi itatu? Kapena m'dziko mwanu mukhale mliri masiku atatu? Chenjerani tsono ndi kulingalira bwino mau amene ine ndibwere nao kwa wonditumayo.


sanaonane, sanaukenso munthu pamalo pake, masiku atatu; koma kwa ana onse a Israele kudayera m'nyumba zao.


Koma Aejipito onse anakumba m'mphepete mwa mtsinje kufuna madzi akumwa; pakuti sanakhoze kumwa madzi a m'mtsinjemo.


Ndipo Yehova anati kwa Mose, Lowa kwa Farao, nunene naye, Atero Yehova, Lola anthu anga amuke, kuti anditumikire.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa