Eksodo 7:24 - Buku Lopatulika24 Koma Aejipito onse anakumba m'mphepete mwa mtsinje kufuna madzi akumwa; pakuti sanakhoze kumwa madzi a m'mtsinjemo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Koma Aejipito onse anakumba m'mphepete mwa nyanja kufuna madzi akumwa; pakuti sanakhoze kumwa madzi a m'nyanjamo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Aejipito onse adayamba kukumba m'mbali mwa mtsinje wa Nailo kuti apeze madzi akumwa, chifukwa sankathanso kumwa madzi a mu mtsinjewo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Anthu onse a ku Igupto anayamba kukumba mʼmbali mwa mtsinje wa Nailo kuti apeze madzi akumwa, chifukwa sanathe kumwa madzi a mu mtsinjemo. Onani mutuwo |