Eksodo 7:18 - Buku Lopatulika18 Ndi nsomba zili m'mtsinje zidzafa, ndi mtsinje idzanunkha; ndi Aejipito adzachita mtima useru ndi kumwa madzi a m'mtsinjemo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndi nsomba zili m'nyanja zidzafa, ndi nyanja idzanunkha; ndi Aejipito adzachita mtima useru ndi kumwa madzi a m'nyanjamo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Nsomba zonse zidzafa, ndipo madziwo adzanunkha, kotere kuti Aejipito sadzafunanso kumwa madzi a mu mtsinje umenewu.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Nsomba za mu Nailo zidzafa, mtsinje udzanunkha ndipo Aigupto sadzatha kumwa madzi ake.’ ” Onani mutuwo |