Eksodo 7:12 - Buku Lopatulika12 Pakuti yense anaponya pansi ndodo yake, ndipo zinasanduka zinjoka; koma ndodo ya Aroni inameza ndodo zao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Pakuti yense anaponya pansi ndodo yake, ndipo zinasanduka zinjoka; koma ndodo ya Aroni inameza ndodo zao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Adaponyanso pansi ndodo zao, ndipo zidasanduka njoka. Koma ndodo ya Aroni ija idameza ndodo zaozo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Aliyense wa iwo anaponya ndodo yake pansi ndipo inasanduka njoka. Koma ndodo ya Aaroni inameza ndodo zawo. Onani mutuwo |