Eksodo 7:12 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Aliyense wa iwo anaponya ndodo yake pansi ndipo inasanduka njoka. Koma ndodo ya Aaroni inameza ndodo zawo. Onani mutuwoBuku Lopatulika12 Pakuti yense anaponya pansi ndodo yake, ndipo zinasanduka zinjoka; koma ndodo ya Aroni inameza ndodo zao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Pakuti yense anaponya pansi ndodo yake, ndipo zinasanduka zinjoka; koma ndodo ya Aroni inameza ndodo zao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Adaponyanso pansi ndodo zao, ndipo zidasanduka njoka. Koma ndodo ya Aroni ija idameza ndodo zaozo. Onani mutuwo |