Eksodo 6:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Mose ananena chomwecho ndi ana a Israele; koma sanamvere Mose chifukwa cha kuwawa mtima, ndi ukapolo wolemera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Mose ananena chomwecho ndi ana a Israele; koma sanamvere Mose chifukwa cha kuwawa mtima, ndi ukapolo wolemera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Mose adauza Aisraele zimenezi, koma iwo sadamvere, chifukwa choti anali atataya kale mtima, pomakhala mu ukapolo wao mwankhalwe chotere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Mose anawafotokozera Aisraeli zimenezi, koma iwo sanamumvere chifukwa cha kukhumudwa ndi goli lankhanza. Onani mutuwo |