Eksodo 6:6 - Buku Lopatulika6 Chifukwa chake nena kwa ana a Israele Ine ndine Yehova, ndipo ndidzakutulutsani pansi pa akatundu a Aejipito ndipo ndidzakulanditsani ku ukapolo wanu; ndipo ndidzakuombolani ndi dzanja lotambasuka, ndi maweruzo aakulu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Chifukwa chake nena kwa ana a Israele Ine ndine Yehova, ndipo ndidzakutulutsani pansi pa akatundu a Aejipito ndipo ndidzakulanditsani ku ukapolo wanu; ndipo ndidzakuombolani ndi dzanja lotambasuka, ndi maweruzo akulu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Tsono iwe ukaŵauze Aisraele mau anga oti, ‘Ine ndine Chauta. Ndidzakutulutsani mu ukapolo wa ntchito yakalavulagaga imene Aejipito akukukakamizani kuigwira. Ndidzakupulumutsani ndi dzanja langa lotambalitsa ndiponso pochita ntchito zamphamvu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 “Nʼchifukwa chake nena kwa Aisraeli kuti, ‘Ine ndine Yehova, ndipo ndidzakutulutsani mʼgoli la Aigupto. Ndidzakumasulani mu ukapolo, ndidzakuwombolani ndi dzanja langa lotambasuka ndi kuchita ntchito zachiweruzo. Onani mutuwo |