Eksodo 6:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Mulungu ananena ndi Mose, nati kwa iye, Ine ndine YEHOVA: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Mulungu ananena ndi Mose, nati kwa iye, Ine ndine YEHOVA: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Mulungu adalankhula ndi Mose namuuza kuti, “Ine ndine Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Mulungu anatinso kwa Mose, “Ine ndine Yehova. Onani mutuwo |