Eksodo 6:15 - Buku Lopatulika15 Ndi ana aamuna a Simeoni ndiwo: Yemuwele, ndi Yamini, ndi Ohadi, Yakini, ndi Zohari, ndi Shaulo mwana wa mkazi wa Mkanani; amenewo ndiwo mabanja a Simeoni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndi ana amuna a Simeoni ndiwo: Yemuwele, ndi Yamini, ndi Ohadi, Yakini, ndi Zohari, ndi Shaulo mwana wa mkazi wa Mkanani; amene ndiwo mabanja a Simeoni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Ana a Simeoni naŵa: Yemuwele, Yamini, Ohadi, Yakini, Zohari ndi Shaulo mwana wa kwa mkazi wa ku Kanani. Ameneŵa ndiwo a m'banja la Simeoni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Ana a Simeoni anali Yemueli, Yamini, Ohadi, Yakini, Zohari ndi Saulo mwana wa kwa mkazi wa Chikanaani. Awa anali mafuko a Simeoni. Onani mutuwo |