Eksodo 5:17 - Buku Lopatulika17 Koma iye anati, Aulesi inu, aulesi: chifukwa chake mulikunena, Timuke, timphere nsembe Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Koma iye anati, Aulesi inu, aulesi: chifukwa chake mulikunena, Timuke, timphere nsembe Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Farao adaŵayankha anthuwo kuti, “Ndinu alesi inu, alesi zedi, nchifukwa chake mukuti, ‘Tiyeni tipite tikapereke nsembe kwa Chauta.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Farao anati, “Ulesi, inu ndinu alesi! Nʼchifukwa chake mukumanena kuti, ‘Mutilole tipite kukapereka nsembe kwa Yehova.’ Onani mutuwo |