Eksodo 5:18 - Buku Lopatulika18 Mukani tsopano, gwirani ntchito; pakuti sadzakupatsani udzu, koma muonetse chiwerengero chake cha njerwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Mukani tsopano, gwirani ntchito; pakuti sadzakupatsani udzu, koma muonetse chiwerengero chake cha njerwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Chokani apa, bwererani ku ntchito yanu. Udzu asakupatseni, koma chiŵerengero cha njerwa ndi chonchija ndithu basi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Pitani tsopano kuntchito. Simudzapatsidwanso udzu komabe muyenera kuwumba muyeso wanu wovomerezeka wa njerwa.” Onani mutuwo |