Eksodo 5:16 - Buku Lopatulika16 Udzu osawapatsa akapolo anu, ndipo amanena ndi ife, Umbani njerwa; ndipo, taonani, amapanda akapolo anu; koma kulakwa nkwa anthu anu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Udzu osawapatsa akapolo anu, ndipo amanena ndi ife, Umbani njerwa; ndipo, taonani, amapanda akapolo anu; koma kulakwa nkwa anthu anu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Udzu satipatsanso ife, bwana, komabe akutilamula kuti, ‘Kaziwumbani njerwa!’ Ndiponso akungotimenya. Anthu anu akulakwa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Antchito anu sakupatsidwa udzu, komabe akutiwuza kuti, ‘Umbani njerwa!’ Antchito anu akumenyedwa, koma cholakwa sichili ndi anthu anu.” Onani mutuwo |