Eksodo 5:15 - Buku Lopatulika15 Pamenepo akapitao a ana a Israele anafika nalirira Farao, nati, Mwatero bwanji ndi akapolo anu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Pamenepo akapitao a ana a Israele anafika nalirira Farao, nati, Mwatero bwanji ndi akapolo anu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Tsono akapitao achiisraele aja adapita kwa Farao kukadandaula kuti, “Pepani amfumu, kaya chifukwa chiyani mwatichita zotere ife atumiki anu? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Pamenepo oyangʼanira anzawo a Chiisraeli aja anapita kukadandaula kwa Farao kuti, “Chifukwa chiyani mwachitira antchito anu zotere? Onani mutuwo |