Eksodo 5:11 - Buku Lopatulika11 Mukani inu nokha, dzifunireni udzu komwe muupeza; pakuti palibe kanthu kadzachepa pa ntchito yanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Mukani inu nokha, dzifunireni udzu komwe muupeza; pakuti palibe kanthu kadzachepa pa ntchito yanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Muzidzimwetera nokha kulikonse komwe mungaupeze. Koma chiŵerengero cha njerwa ndi chonchija.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Mʼmalo mwake mupite mukadzimwetere udzu kulikonse kumene mungawupeze. Komabe ntchito yanu sichepetsedwa.’ ” Onani mutuwo |