Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 5:11 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Mʼmalo mwake mupite mukadzimwetere udzu kulikonse kumene mungawupeze. Komabe ntchito yanu sichepetsedwa.’ ”

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

11 Mukani inu nokha, dzifunireni udzu komwe muupeza; pakuti palibe kanthu kadzachepa pa ntchito yanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Mukani inu nokha, dzifunireni udzu komwe muupeza; pakuti palibe kanthu kadzachepa pa ntchito yanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Muzidzimwetera nokha kulikonse komwe mungaupeze. Koma chiŵerengero cha njerwa ndi chonchija.’ ”

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 5:11
3 Mawu Ofanana  

Choncho akapitawo a thangata ndi anzawo a Chiisraeli amene ankayangʼanira anthu anapita kwa anthu aja nati, “ ‘Farao akuti sadzakupatsaninso udzu.


Kotero anthuwo anamwazikana mʼdziko lonse la Igupto kukamweta udzu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa