Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 40:32 - Buku Lopatulika

32 pakulowa iwo m'chihema chokomanako, ndi pakuyandikiza guwa la nsembe anasamba; monga Yehova adamuuza Mose.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 pakulowa iwo m'chihema chokomanako, ndi pakuyandikiza guwa la nsembe anasamba; monga Yehova adamuuza Mose.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 Nthaŵi zonse akaloŵa m'chihema chamsonkhanomo, kapena kusendera ku guwalo, ankasamba, monga momwe Chauta adalamulira Mose.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 Iwo amasamba nthawi zonse akamalowa mu tenti ya msonkhano kapena kuyandikira guwa lansembe monga Yehova analamulira Mose.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 40:32
7 Mawu Ofanana  

Ha? M'kamphindi ayesedwa bwinja; athedwa konse ndi zoopsa.


Ndipo ubwere nao Aroni ndi ana ake aamuna ku khomo la chihema chokomanako, ndi kuwasambitsa m'madzi.


Ndipo anayalika hema pamwamba pa Kachisi, naika chophimba cha chihema pamwamba pake; monga Yehova adamuuza Mose.


Ndipo Mose ndi Aroni ndi ana ake aamuna anasamba manja ao ndi mapazi ao m'menemo;


Ndipo anautsa mpanda pozungulira pa chihema ndi guwa la nsembe, napachika nsalu yotsekera pa chipata cha pabwalo. Momwemo Mose anatsiriza ntchitoyi.


Monga Yehova analamula Mose, momwemo anawawerenga m'chipululu cha Sinai.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa