Eksodo 40:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo Mose ndi Aroni ndi ana ake aamuna anasamba manja ao ndi mapazi ao m'menemo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo Mose ndi Aroni ndi ana ake amuna anasamba manja ao ndi mapazi ao m'menemo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Apo Mose, Aroni ndi ana ake adasamba m'manja natsuka mapazi ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 ndipo Mose, Aaroni ndi ana ake amasamba manja ndi mapazi awo. Onani mutuwo |