Eksodo 40:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo anaika mkhate pakati pa chihema chokomanako, ndi guwa la nsembe; nathiramo madzi osamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo anaika mkhate pakati pa chihema chokomanako, ndi guwa la nsembe; nathiramo madzi osamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Kenaka adaika beseni losambira lija pakati pa chihema chamsonkano ndi guwa, nathiramo madzi osamba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Iye anayika beseni pakati pa tenti ya msonkhano ndi guwa lansembe ndipo anathiramo madzi wosamba, Onani mutuwo |