Eksodo 40:33 - Buku Lopatulika33 Ndipo anautsa mpanda pozungulira pa chihema ndi guwa la nsembe, napachika nsalu yotsekera pa chipata cha pabwalo. Momwemo Mose anatsiriza ntchitoyi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ndipo anautsa mpanda pozungulira pa chihema ndi guwa la nsembe, napachika nsalu yotsekera pa chipata cha pabwalo. Momwemo Mose anatsiriza ntchitoyi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Adamanga bwalo lonse lozungulira chihema chija ndi guwa. Adaikanso nsalu yochinga pa chipata cha bwalolo. Motero Mose adamaliza ntchito yonseyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Kenaka Mose anamanga bwalo kuzungulira chihema ndi guwa lansembe ndipo anayika katani ya pa chipata cha bwalo. Kotero Mose anamaliza ntchito. Onani mutuwo |