Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 40:27 - Buku Lopatulika

27 nafukizapo chofukiza cha fungo lokoma; monga Yehova adamuuza Mose.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

27 nafukizapo chofukiza cha fungo lokoma; monga Yehova adamuuza Mose.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

27 Adafukiza lubani wa fungo lokoma paguwapo, monga momwe Chauta adamlamulira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

27 ndipo anapserezapo lubani wonunkhira monga Yehova anamulamulira.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 40:27
2 Mawu Ofanana  

Ndipo Aroni azifukizapo chofukiza cha zonunkhira zokoma m'mawa ndi m'mawa, pamene akonza nyalizo, achifukize.


Ndipo anapachika pa chihema nsalu yotsekera pakhomo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa