Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 40:28 - Buku Lopatulika

28 Ndipo anapachika pa chihema nsalu yotsekera pakhomo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

28 Ndipo anapachika ku Kachisi nsalu yotsekera pakhomo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

28 Pa khomo la malo opatulika adaikapo nsalu yochinga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

28 Kenaka anayika katani ya pa chipata cha chihema.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 40:28
9 Mawu Ofanana  

nafukizapo chofukiza cha fungo lokoma; monga Yehova adamuuza Mose.


Ndipo anaika guwa la nsembe yopsereza pa khomo la Kachisi wa chihema chokomanako, natenthapo nsembe yopsereza, ndi nsembe yaufa; monga Yehova adamuuza Mose.


Ndipo ukaike guwa la nsembe lofukizapo lagolide chakuno cha likasa la mboni, numange pa chihema nsalu yotsekera pakhomo.


Ine ndine khomo; ngati wina alowa ndi Ine, adzapulumutsidwa, nadzalowa, nadzatuluka, nadzapeza busa.


Yesu ananena naye, Ine ndine njira, ndi choonadi, ndi moyo. Palibe munthu adza kwa Atate, koma mwa Ine.


kuti mwa Iye ife tonse awiri tili nao malowedwe athu kwa Atate, mwa Mzimu mmodzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa