Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 40:26 - Buku Lopatulika

26 Ndipo anaika guwa la nsembe lagolide m'chihema chokomanako chakuno cha nsalu yotchinga;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 Ndipo anaika guwa la nsembe lagolide m'chihema chokomanako chakuno cha nsalu yotchinga;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 M'chihema chamsonkhanomo adaikamo guwa lagolide patsogolo pa nsalu yochinga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 Mose anayika guwa la golide mu tenti ya msonkhano patsogolo pa katani

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 40:26
9 Mawu Ofanana  

Ndipo ukaike guwa la nsembe lofukizapo lagolide chakuno cha likasa la mboni, numange pa chihema nsalu yotsekera pakhomo.


ndipo wansembeyo aviike chala chake m'mwazimo, nawaze mwaziwo kasanu ndi kawiri pamaso pa Yehova chakuno cha nsalu yotchinga, ya malo opatulika.


Inu akhungu, pakuti choposa nchiti, mtulo kodi, kapena guwa la nsembe limene liyeretsa mtulowo?


Koma ndadziwa Ine kuti mumandimva Ine nthawi zonse; koma chifukwa cha khamu la anthu alikuimirira pozungulira ndinanena ichi, kuti akhulupirire kuti Inu munandituma Ine.


Pakuti chilamulo, pokhala nao mthunzi wa zokoma zilinkudza, osati chifaniziro chenicheni cha zinthuzo, sichikhozatu, ndi nsembe zomwezi chaka ndi chaka, zimene azipereka kosalekeza, kuwayesera angwiro iwo akuyandikira.


kuchokera komweko akhoza kupulumutsa konsekonse iwo akuyandikira kwa Mulungu mwa Iye, popeza ali nao moyo wake chikhalire wa kuwapembedzera iwo.


Tiana tanga, izi ndikulemberani, kuti musachimwe. Ndipo akachimwa wina, Nkhoswe tili naye kwa Atate, ndiye Yesu Khristu wolungama;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa