Eksodo 40:25 - Buku Lopatulika25 Nayatsa nyalizo pamaso pa Yehova; monga Yehova adamuuza Mose. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Nayatsa nyalizo pamaso pa Yehova; monga Yehova adamuuza Mose. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Tsono pa choikaponyalecho adaikapo nyale, kuti zikhale pamaso pa Chauta, monga momwe Iye adalamulira Mose. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Ndipo anayikapo nyale zija pamaso pa Yehova, monga Yehova analamulira Mose. Onani mutuwo |