Eksodo 40:21 - Buku Lopatulika21 nalowa nalo likasa mu chihema, napachika nsalu yotchinga, natchinga likasa la mboni; monga Yehova adamuuza Mose. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 nalowa nalo likasa m'Kachisi, napachika nsalu yotchinga, natchinga likasa la mboni; monga Yehova adamuuza Mose. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Kenaka adaika bokosilo m'malo opatulika, ndipo adaika nsalu zochingira. Motero adachinga bokosi laumboni, monga momwe Chauta adamlamulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Kenaka analowetsa bokosilo mʼchihema ndipo anapachika katani ndi kubisa bokosi la umboni monga momwe Yehova analamulira iye. Onani mutuwo |