Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 40:22 - Buku Lopatulika

22 Ndipo anaika gomelo m'chihema chokomanako, pa mbali ya kumpoto ya Kachisi, kunja kwa nsalu yotchinga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Ndipo anaika gomelo m'chihema chokomanako, pa mbali ya kumpoto ya Kachisi, kunja kwa nsalu yotchinga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Tsono m'chihema chamsonkhanomo adaikamo tebulo, chakumpoto kwa malo opatulika, kunja kwa nsalu yochinga ija,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Mose anayika tebulo mu tenti ya msonkhano kumpoto kwa chihema, kunja kwa katani,

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 40:22
5 Mawu Ofanana  

Nuziika gomelo kunja kwa nsalu yotchinga, ndi choikaponyali pandunji pa gome, pa mbali ya kumwera ya chihema; koma uike gomelo pa mbali ya kumpoto.


Ndipo anaika choikaponyali m'chihema chokomanako, popenyana ndi gome, pa mbali ya kumwera ya Kachisi.


Ulongenso gomelo, nukonzerepo zokonzera zake; ulongenso choikaponyalicho, ndi kuyatsa nyali zake.


Kwa ine wochepa ndi wochepetsa wa onse oyera mtima anandipatsa chisomo ichi ndilalikire kwa amitundu chuma chosalondoleka cha Khristu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa