Eksodo 40:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo anatenga mboniyo, naiika m'likasa, napisa mphiko palikasa, naika chotetezerapo pamwamba pa likasa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo anatenga mboniyo, naiika m'likasa, napisa mphiko palikasa, naika chotetezerapo pamwamba pa likasa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Tsono adatenga miyala yaumboni ija naiika m'bokosi muja. Adapisa mphiko zija m'mphete za bokosilo, naika chivundikiro pamwamba pake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Iye anatenga miyala ya umboni nayika mʼbokosi lija ndi kuyika chivundikiro pamwamba pake. Onani mutuwo |