Eksodo 40:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo anayalika hema pamwamba pa Kachisi, naika chophimba cha chihema pamwamba pake; monga Yehova adamuuza Mose. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo anayalika hema pamwamba pa Kachisi, naika chophimba cha chihema pamwamba pake; monga Yehova adamuuza Mose. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Pambuyo pake adautsa chihema pamwamba pa malo opatulikawo, nachiphimba ndi chophimbira chake cha chihema, monga momwe Chauta adamlamulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Kenaka anayika tenti pamwamba pa chihema ndipo anayika chophimba pa tenti monga momwe Yehova analamulira Mose. Onani mutuwo |