Eksodo 40:18 - Buku Lopatulika18 ndipo Mose anautsa chihema, nakhazika makamwa ake, naimika matabwa ake, namangapo mitanda yake, nautsa mizati ndi nsanamira zake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 ndipo Mose anautsa Kachisi, nakhazika makamwa ake, naimika matabwa ake, namangapo mitanda yake, nautsa mizati ndi nsanamira zake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Poutsa malowo, Mose adakhazika masinde ake pansi, ndipo adautsa mafulemu ake, nalumikiza mitanda yake, nautsanso nsanamira zake zija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Nthawi imene Mose anayimika chihema, anayika matsinde mʼmalo ake, kuyimitsa maferemu, kulowetsa mitanda ndi kuyika nsichi. Onani mutuwo |