Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 40:17 - Buku Lopatulika

17 Ndipo kunali, mwezi woyamba wa chaka chachiwiri, tsiku loyamba la mwezi, anautsa chihema,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Ndipo kunali, mwezi woyamba wa chaka chachiwiri, tsiku loyamba la mwezi, anautsa Kachisi,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Motero pa tsiku loyamba la mwezi woyamba chaka chachiŵiri, malo opatulika adautsidwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Kotero anayimika chihema tsiku loyamba la mwezi woyamba mʼchaka chachiwiri.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 40:17
9 Mawu Ofanana  

Mwezi uno uzikhala kwa inu woyamba wa miyezi; muziuyesa mwezi woyamba wa chaka.


Anatero Mose; monga mwa zonse Yehova adamuuza, momwemo anachita.


ndipo Mose anautsa chihema, nakhazika makamwa ake, naimika matabwa ake, namangapo mitanda yake, nautsa mizati ndi nsanamira zake.


Ndipo Yehova ananena ndi Mose m'chipululu cha Sinai, m'chihema chokomanako, tsiku loyamba la mwezi wachiwiri, chaka chachiwiri atatuluka m'dziko la Ejipito, ndi kuti,


Ndipo kunachitika, chaka chachiwiri, mwezi wachiwiri, tsiku la makumi awiri la mweziwo, kuti mtambo unakwera kuchokera kwa chihema cha mboni.


Ndipo kunali kuti tsiku lomwe Mose anatsiriza kuutsa chihema, nachidzoza ndi kuchipatula, ndi zipangizo zake zonse, ndi guwa la nsembe, ndi zipangizo zake zonse, nazidzoza ndi kuzipatula;


Ndipo Yehova ananena ndi Mose m'chipululu cha Sinai, mwezi woyamba wa chaka chachiwiri atatuluka m'dziko la Ejipito, ndi kuti,


Ndipo tsiku loutsa Kachisi mtambo unaphimba Kachisi, ndiwo chihema chokomanako; ndicho chihema chaumboni, ndipo madzulo padaoneka pa Kachisi ngati moto, kufikira m'mawa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa