Eksodo 40:16 - Buku Lopatulika16 Anatero Mose; monga mwa zonse Yehova adamuuza, momwemo anachita. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Anatero Mose; monga mwa zonse Yehova adamuuza, momwemo anachita. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Mose adachita zonse, monga momwe Chauta adamlamulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Mose anachita zonse monga Yehova anamulamulira. Onani mutuwo |