Eksodo 40:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo ubwere nao Aroni ndi ana ake aamuna ku khomo la chihema chokomanako, ndi kuwasambitsa ndi madzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo ubwere nao Aroni ndi ana ake amuna ku khomo la chihema chokomanako, ndi kuwasambitsa ndi madzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 “Pambuyo pake ubwere ndi Aroni ku chipata cha chihema chamsonkhano, pamodzi ndi ana ake omwe, ndipo onsewo asambe kumeneko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 “Ubwere ndi Aaroni ndi ana ake pa chipata cha tenti ya msonkhano ndipo uwasambitse ndi madzi. Onani mutuwo |