Eksodo 40:11 - Buku Lopatulika11 Udzozenso mkhate ndi tsinde lake, ndi kuupatula. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Udzozenso mkhate ndi tsinde lake, ndi kuupatula. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Udzoze beseni losambira, pamodzi ndi phaka lake lomwe, ndipo ulipereke kwa Mulungu, kuti likhale loyera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Udzoze beseni ndi miyendo yake ndipo uzipatule. Onani mutuwo |