Eksodo 39:36 - Buku Lopatulika36 gomelo, zipangizo zake zonse, ndi mkate woonekera; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 gomelo, zipangizo zake zonse, ndi mkate woonekera; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Adabweranso ndi tebulo, pamodzi ndi zipangizo zake, ndipo adaika buledi woperekedwa kosalekeza kwa Mulungu; Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 tebulo pamodzi ndi zipangizo zake ndiponso buledi wokhala pamaso pa Yehova; Onani mutuwo |