Eksodo 39:37 - Buku Lopatulika37 choikaponyali choona, nyali zake, ndizo nyali zimakonzekazi, ndi zipangizo zake zonse, ndi mafuta a kuunikira; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201437 choikapo nyali choona, nyali zake, ndizo nyali zimakonzekazi, ndi zipangizo zake zonse, ndi mafuta a kuunikira; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa37 choikaponyale cha golide wabwino kwambiri, nyale zake pamodzi ndi zipangizo zake, mafuta anyale; Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero37 choyikapo nyale chagolide wabwino kwambiri pamodzi ndi nyale zake ndi zipangizo zake zonse, ndiponso mafuta anyalezo; Onani mutuwo |