Eksodo 39:35 - Buku Lopatulika35 likasa la mboni, ndi mphiko zake, ndi chotetezerapo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 likasa la mboni, ndi mphiko zake, ndi chotetezerapo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 bokosi loikamo miyala yaumboni pamodzi ndi nsanamira zake, ndiponso chivundikiro cha bokosilo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 bokosi la umboni pamodzi ndi mitengo yake yonyamulira ndiponso chovundikira chake; Onani mutuwo |