Eksodo 39:34 - Buku Lopatulika34 ndi chophimba cha zikopa za nkhosa zamphongo zonyika zofiirira, ndi chophimba cha zikopa za akatumbu, ndi nsalu yotchinga yotsekera; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 ndi chophimba cha zikopa za nkhosa zamphongo zonika zofiira, ndi chophimba cha zikopa za akatumbu, ndi nsalu yotchinga yotsekera; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Adabweranso ndi chophimbira cha chikopa chankhosa chonyika mu utoto wofiira, chophimbira cha chikopa chambuzi, nsalu zochingira, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 chophimba cha chikopa cha nkhosa yayimuna chonyikidwa mu utoto ofiira, chophimba cha chikopa cha akatumbu ndi nsalu zophimba; Onani mutuwo |