Eksodo 39:33 - Buku Lopatulika33 Ndipo anabwera naye Kachisi kwa Mose, chihemacho, ndi zipangizo zake zonse, zokowera zake, matabwa ake, mitanda yake, ndi mizati yake, nsanamira zake ndi nsichi zake, ndi makamwa ake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ndipo anabwera naye Kachisi kwa Mose, chihemacho, ndi zipangizo zake zonse, zokowera zake, matabwa ake, mitanda yake, ndi mizati yake, nsanamira zake ndi nsichi zake, ndi makamwa ake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Pambuyo pake zonsezo adabwera nazo kwa Mose: chihema chija chodzakhala Nyumba ya Mulungu, pamodzi ndi zipangizo zake zonse, ngoŵe zake zokoŵera, mafulemu ake, mitanda yake, nsanamira zake ndi masinde ake omwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Kenaka anabweretsa chihema kwa Mose. Tenti ndi zipangizo zake, ngowe zake, maferemu ake, mitanda yake, mizati yake ndi matsinde ake; Onani mutuwo |