Eksodo 39:32 - Buku Lopatulika32 Potero anatsiriza ntchito yonse ya Kachisi wa chihema chokomanako; ndipo ana a Israele adachita monga mwa zonse Yehova adamuuza Mose, anachita momwemo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Potero anatsiriza ntchito yonse ya Kachisi wa chihema chokomanako; ndipo ana a Israele adachita monga mwa zonse Yehova adamuuza Mose, anachita momwemo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Tsono ntchito yonse yomanga chihema chamsonkhano idatha. Aisraele aja adachitadi zonse, monga momwe Chauta adalamulira Mose. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Tsopano ntchito yonse ya tenti ya msonkhano inatha. Aisraeli anachita zonse monga momwe Yehova analamulira Mose. Onani mutuwo |