Eksodo 39:31 - Buku Lopatulika31 Namangako mkuzi wamadzi, kuumanga nao pamwamba pa nduwira; monga Yehova adamuuza Mose. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Namangako mkuzi wamadzi, kuumanga nao pamwamba pa nduwira; monga Yehova adamuuza Mose. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Kenaka adatenga kamkuzi kobiriŵira namangirira duŵa limenelo ku nsalu ya nduŵira ija, monga momwe Chauta adalamulira Mose. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Kenaka analimangira ndi chingwe cha nsalu yamtundu wa mtambo pa nduwira, monga momwe Yehova analamulira Mose. Onani mutuwo |