Eksodo 39:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo anapanga phanthiphanthi wa korona wopatulika wa golide woona, nalembapo lemba, ngati malochedwe a chosindikizira, KUPATULIKIRA YEHOVA. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo anapanga phanthiphanthi wa korona wopatulika wa golide woona, nalembapo lemba, ngati malochedwe a chosindikizira, KUPATULIKIRA YEHOVA. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Ndipo adapanga duŵa la golide wabwino kwambiri. Limenelo linali chizindikiro chopatulika, ndipo mofanizira ndi mazokotedwe a chidindo, adazokotapo mau akuti, “Chopereka kwa Chauta.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Iwo anapanga duwa lagolide wabwino kwambiri ngati chidindo ndipo anazokotapo mawu akuti, wopatulikira Yehova. Onani mutuwo |